Skip survey header
Chichewa

Kuyesera: InCommon Insights

Ichi ndi chitsanzo cha kafukufuku omwe mafunso ake tikufuna kufunsa mipingo pa kafukufuku wa InCommon Insights. Mukhoza kuyang'ana kafukufukuyu kuti mudziwe zambiri makamaka zolinga zake, mafunso ake, komanso momwe wapangidwira. SI kafukufuku weniweni ndipo asatumizidwe kwa mipingo.

-------


Zikomo potenga nthawi yochepa kuti mutigawile zokhudza utumiki wa ana, achinyamata, ndi mabanja ku mpingo wanu. Ntchitoyi itithandiza kuti timvetse bwino momwe mipingo ikuugwilira ntchito ya utumikuwu mtsogolo.

Mtsogoleri wa mpingo amene amadziwa zambiri zokhudza utumiki wa ana ndi achinyamata ndiye ayenera kuyankha mafuso awa. Mpingo uliwonse uyenera kuyankha fomu imodzi yokha. Zititengela pafupifupi mphindi 15. Yankhani mogwirizana ndi mpingo wanu.

Mafunsowa akufuna kudziwa zambiri ndi mmene mpingo wanu ukuchitila ku mzati zisanu zopitisa utumiku patsogolo:

  • Kukuza Utumiki

  • Atsogoleri Oyenerera

  • Zipangizo Zabwino

  • Masomphenya Olimbikitsa

  • Mitundu Ya Utumiki Yofunika

 

Pomaliza, zotsatira za kafukufuku zimaperekedwa pa gawo lililonse. Chida ichi chapangidwa kuti chithandize pakuuinikila ndi kukuuza utumiki. Chonde yankhani moona mtima. Zomwe muyankhe zikhala zachinsinsi. Zikomo kwambiri chifukwa cha nthawi yanu!

Dziko:
This question requires a valid email address.